Mode za kuwerengera
Batani lamtundu wa masamu limasankha mtundu wa masamu. Dinani
kenako
kuti mupeze COMP, mtundu wa masamu wamba, mmene timachitira pafupifupi zonse. Dinani
ndi
kuti mupeze STAT, mtundu wa sitatisitiki, imene imayamba ndi kufunsa mtundu wa masamu. Ndipo
ndi
ndi TABLE, imene imapanga tebulo la mitengo kuchokera ku fankishoni. Tibwerera ku STAT ndi TABLE mu Gawo 6.